-
Mateyu 18:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tsoka kwa dzikoli chifukwa cha zopunthwitsa! Inde sitingachitire mwina, zopunthwitsazo ziyenera kubwera ndithu, koma tsoka kwa munthu wobweretsa chopunthwitsa!
-