Mateyu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mukuganiza bwanji? Ngati munthu ali ndi nkhosa 100 ndipo imodzi mwa nkhosazo nʼkusochera,+ kodi sangasiye nkhosa 99 zija mʼphiri nʼkupita kukafunafuna yosocherayo?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),6/2020, ptsa. 19-20 Nsanja ya Olonda,2/1/2008, tsa. 10
12 Mukuganiza bwanji? Ngati munthu ali ndi nkhosa 100 ndipo imodzi mwa nkhosazo nʼkusochera,+ kodi sangasiye nkhosa 99 zija mʼphiri nʼkupita kukafunafuna yosocherayo?+