-
Mateyu 18:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndithu ndikukuuzani, zilizonse zimene mudzamange padziko lapansi zidzakhala zoti zamangidwa kale kumwamba. Ndipo zilizonse zimene mudzamasule padziko lapansi zidzakhala zoti zamasulidwa kale kumwamba.
-