Mateyu 18:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiponso ndikukuuzani kuti, ngati awiri mwa inu padziko lapansi pano mutagwirizana kuti mupemphe chinthu chilichonse chofunika, Atate wanga wakumwamba adzakuchitirani.+
19 Ndiponso ndikukuuzani kuti, ngati awiri mwa inu padziko lapansi pano mutagwirizana kuti mupemphe chinthu chilichonse chofunika, Atate wanga wakumwamba adzakuchitirani.+