-
Mateyu 18:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno kapoloyu anagwada pansi nʼkumuweramira ndipo ananena kuti, ‘Ndilezereni mtima chonde, ndidzakubwezerani zonse.’
-