Mateyu 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma kapolo ameneyu atatuluka anakumana ndi kapolo mnzake amene anali ndi ngongole yake yokwana madinari 100.* Choncho anamugwira nʼkuyamba kumukanyanga pakhosi, akunena kuti, ‘Bweza ngongole ija mwamsanga.’ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:28 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 9
28 Koma kapolo ameneyu atatuluka anakumana ndi kapolo mnzake amene anali ndi ngongole yake yokwana madinari 100.* Choncho anamugwira nʼkuyamba kumukanyanga pakhosi, akunena kuti, ‘Bweza ngongole ija mwamsanga.’