-
Mateyu 18:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ndiyeno mbuye wakeyo anamuitanitsa nʼkumuuza kuti: ‘Kapolo woipa iwe, ine ndakukhululukira ngongole yonse ija utandidandaulira.
-