Mateyu 18:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Atate wanga wakumwamba adzakuchitiraninso zofanana ndi zimenezi+ ngati aliyense wa inu sakhululukira mʼbale wake ndi mtima wonse.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:35 Yesu—Ndi Njira, tsa. 153 Nsanja ya Olonda,3/1/1988, tsa. 9
35 Atate wanga wakumwamba adzakuchitiraninso zofanana ndi zimenezi+ ngati aliyense wa inu sakhululukira mʼbale wake ndi mtima wonse.”+