Mateyu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Afarisi anabwera kwa iye nʼcholinga chodzamuyesa ndipo anamufunsa kuti: “Kodi mwamuna ali ndi ufulu wothetsa banja ndi mkazi wake pa chifukwa chilichonse?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:3 Yesu—Ndi Njira, tsa. 222 Nsanja ya Olonda,8/15/1993, ptsa. 4-57/15/1989, tsa. 8
3 Ndiyeno Afarisi anabwera kwa iye nʼcholinga chodzamuyesa ndipo anamufunsa kuti: “Kodi mwamuna ali ndi ufulu wothetsa banja ndi mkazi wake pa chifukwa chilichonse?”+