Mateyu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukundifunsa zokhudza zinthu zabwino? Pali mmodzi yekha amene ndi wabwino.+ Choncho ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:17 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, tsa. 86/15/1986, ptsa. 8-9
17 Iye anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukundifunsa zokhudza zinthu zabwino? Pali mmodzi yekha amene ndi wabwino.+ Choncho ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+