Mateyu 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anafunsa kuti: “Malamulo ake ati?” Yesu anayankha kuti: “Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza.+
18 Iye anafunsa kuti: “Malamulo ake ati?” Yesu anayankha kuti: “Musaphe munthu,*+ musachite chigololo,+ musabe,+ musapereke umboni wabodza.+