Mateyu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu,+ komanso lakuti, Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:19 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2019, ptsa. 24-25
19 Muzilemekeza bambo anu ndi mayi anu,+ komanso lakuti, Uzikonda mnzako mmene umadzikondera wekha.”+