Mateyu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Ufumu wakumwamba uli ngati munthu amene anali ndi munda wa mpesa, amene analawirira mʼmawa kwambiri kukafuna anthu aganyu kuti akagwire ntchito mʼmunda wake wa mpesa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:1 Yesu—Ndi Njira, tsa. 226 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, tsa. 8
20 “Ufumu wakumwamba uli ngati munthu amene anali ndi munda wa mpesa, amene analawirira mʼmawa kwambiri kukafuna anthu aganyu kuti akagwire ntchito mʼmunda wake wa mpesa.+