-
Mateyu 20:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iwo anamuyankha kuti, ‘Chifukwa palibe amene watilemba ganyu.’ Iye anawauza kuti, ‘Inunso pitani mukagwire ntchito kumunda wanga wa mpesa.’
-