Mateyu 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho oyambirira aja atafika, anaganiza kuti alandira zambiri, koma nawonso malipiro amene analandira anali dinari* imodzi. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2242 Nsanja ya Olonda,8/15/1989, ptsa. 8-9
10 Choncho oyambirira aja atafika, anaganiza kuti alandira zambiri, koma nawonso malipiro amene analandira anali dinari* imodzi.