Mateyu 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma poyankha kwa mmodzi wa iwo, mwinimundayo anati, ‘Bwanawe, sindinakulakwire. Tinapangana malipiro a dinari* imodzi, si choncho?+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:13 Nsanja ya Olonda,8/1/2010, ptsa. 29-30
13 Koma poyankha kwa mmodzi wa iwo, mwinimundayo anati, ‘Bwanawe, sindinakulakwire. Tinapangana malipiro a dinari* imodzi, si choncho?+