Mateyu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yesu anayankha kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndatsala pangʼono kumwa?”+ Iwo anayankha kuti: “Inde tingamwe.” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 229 Nsanja ya Olonda,9/1/1989, tsa. 8
22 Yesu anayankha kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe zimene ine ndatsala pangʼono kumwa?”+ Iwo anayankha kuti: “Inde tingamwe.”