-
Mateyu 20:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndiye gulu la anthulo linawakalipira nʼkuwauza kuti akhale chete. Koma mʼpamene iwo anafuula kwambiri kuti: “Ambuye, Mwana wa Davide, tichitireni chifundo!”
-