Mateyu 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso gulu la anthu limene linali patsogolo pake ndi mʼmbuyo mwake linkafuula kuti: “Mʼpulumutseni Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+ Mʼpulumutseni kumwambamwambako!”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, tsa. 9 Nsanja ya Olonda,3/1/1997, ptsa. 30-31
9 Komanso gulu la anthu limene linali patsogolo pake ndi mʼmbuyo mwake linkafuula kuti: “Mʼpulumutseni Mwana wa Davide!+ Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova!*+ Mʼpulumutseni kumwambamwambako!”+