Mateyu 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ndipo anamufunsa kuti: “Kodi ukumva zimene anthu akunenazi?” Yesu anayankha kuti: “Inde. Kodi simunawerenge zimenezi kuti, ‘Mwachititsa kuti mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda mutuluke mawu otamandaʼ?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:16 “Wotsatira Wanga,” ptsa. 101-102 Nsanja ya Olonda,1/1/1995, ptsa. 24-26
16 ndipo anamufunsa kuti: “Kodi ukumva zimene anthu akunenazi?” Yesu anayankha kuti: “Inde. Kodi simunawerenge zimenezi kuti, ‘Mwachititsa kuti mʼkamwa mwa ana ndi mwa makanda mutuluke mawu otamandaʼ?”+