Mateyu 21:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yesu atalowa mʼkachisi nʼkumaphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndi ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 244 Nsanja ya Olonda,1/15/1999, ptsa. 25-2612/15/1989, tsa. 8
23 Yesu atalowa mʼkachisi nʼkumaphunzitsa, ansembe aakulu ndiponso akulu anabwera kwa iye nʼkumufunsa kuti: “Kodi muli ndi ulamuliro wochitira zinthu zimenezi? Ndipo ndi ndani amene anakupatsani ulamuliro umenewu?”+