Mateyu 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kodi ubatizo umene Yohane ankachita unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?” Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga nʼchifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+
25 Kodi ubatizo umene Yohane ankachita unachokera kuti? Kumwamba kapena kwa anthu?” Koma iwo anayamba kukambirana kuti: “Tikanena kuti, ‘Unachokera kumwamba,’ atifunsa kuti, ‘Nanga nʼchifukwa chiyani simunamukhulupirire?’+