-
Mateyu 21:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Choncho iwo anayankha Yesu kuti: “Sitikudziwa.” Nayenso anawauza kuti: “Inenso sindikuuzani amene anandipatsa ulamuliro umene ndimachitira zimenezi.
-