-
Mateyu 21:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Kodi mukuganiza bwanji? Munthu wina anali ndi ana awiri. Ndipo anapita kwa mwana woyamba nʼkumuuza kuti, ‘Mwana wanga, lero upite kukagwira ntchito mʼmunda wa mpesa.’
-