-
Mateyu 21:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Ndi ndani mwa ana awiriwa amene anachita zimene bambo ake ankafuna?” Iwo anayankha kuti: “Woyambayo.” Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani kuti okhometsa msonkho ndiponso mahule akukusiyani mʼmbuyo nʼkukalowa mu Ufumu wa Mulungu.
-