Mateyu 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa Yohane anabwera kwa inu kudzakuphunzitsani njira yachilungamo, koma inu simunamukhulupirire. Koma okhometsa msonkho ndi mahule anamukhulupirira.+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunasinthe maganizo anu nʼkuyamba kumukhulupirira.
32 Chifukwa Yohane anabwera kwa inu kudzakuphunzitsani njira yachilungamo, koma inu simunamukhulupirire. Koma okhometsa msonkho ndi mahule anamukhulupirira.+ Ngakhale kuti inu munaona zimenezi, simunasinthe maganizo anu nʼkuyamba kumukhulupirira.