Mateyu 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mvetserani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ nʼkumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa nʼkumanga nsanja.+ Atatero anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 246 Nsanja ya Olonda,1/1/1990, tsa. 8
33 Mvetserani fanizo lina: Panali munthu wina yemwe analima munda wa mpesa+ nʼkumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa nʼkumanga nsanja.+ Atatero anausiya mʼmanja mwa alimi nʼkupita kudziko lina.+