-
Mateyu 21:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angamupatse zipatso mʼnyengo yake.”
-