Mateyu 21:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ? Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:42 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 246-247
42 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Paja Malemba amanena kuti, ‘Mwala umene omanga nyumba anaukana wakhala mwala wapakona wofunika kwambiri.*+ Umenewu wachokera kwa Yehova* ndipo ndi wodabwitsa mʼmaso mwathu.+ Kodi simunawerenge zimeneziʼ?