Mateyu 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zitatero mfumu ija inakwiya kwambiri ndipo inatumiza asilikali ake kukapha anthu amene anapha akapolo akewo nʼkuwotcha mzinda wawo.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:7 Yesu—Ndi Njira, tsa. 249 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, ptsa. 8-9
7 Zitatero mfumu ija inakwiya kwambiri ndipo inatumiza asilikali ake kukapha anthu amene anapha akapolo akewo nʼkuwotcha mzinda wawo.+