-
Mateyu 22:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ndiyeno akapolowo anapita mʼmisewu ndipo anasonkhanitsa onse amene anawapeza, oipa ndi abwino omwe. Ndipo chipinda chodyeramo phwando laukwati chinadzaza ndi anthu amene ankadya chakudya.
-