-
Mateyu 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako mfumuyo inauza atumiki ake kuti, ‘Mʼmangeni manja ndi miyendo ndipo mumuponye kunja kumdima. Kumeneko akalira ndi kukukuta mano.’
-