Mateyu 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Afarisi anachoka nʼkukapangana kuti amupezere zifukwa pa zimene angalankhule.+