-
Mateyu 22:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Choncho anamutumizira ophunzira awo, limodzi ndi anthu amene ankatsatira Herode,+ ndipo iwo ananena kuti: “Mphunzitsi, tikudziwa kuti inu mumanena zoona ndipo mumaphunzitsa njira ya Mulungu mʼchoonadi, ndiponso simuchita zinthu pongofuna kusangalatsa munthu, chifukwa simuyangʼana maonekedwe a anthu.
-