Mateyu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiye tatiuzani, mukuganiza bwanji? Kodi nʼzololeka* kupereka msonkho kwa Kaisara kapena ayi?” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:17 Yesu—Ndi Njira, tsa. 250 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, tsa. 8