Mateyu 22:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndionetseni khobidi la msonkho.” Iwo anamubweretsera khobidi limodzi la dinari.*