Mateyu 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pa tsiku limenelo Asaduki amene amanena kuti akufa sadzaukitsidwa,+ anabwera nʼkumufunsa kuti:+