-
Mateyu 22:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Tsopano panali amuna 7 apachibale. Woyamba anakwatira kenako nʼkumwalira. Koma popeza kuti analibe ana, mkaziyo anakwatiwa ndi mchimwene wa mwamuna wake uja.
-