Mateyu 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chifukwa akufa akadzaukitsidwa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa, koma adzakhala ngati angelo akumwamba.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:30 Nsanja ya Olonda,6/1/1987, ptsa. 30-31
30 Chifukwa akufa akadzaukitsidwa, amuna sadzakwatira ndipo akazi sadzakwatiwa, koma adzakhala ngati angelo akumwamba.+