Mateyu 22:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Gulu la anthulo litamva zimenezo, linadabwa ndi zimene ankaphunzitsa.+