-
Mateyu 22:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Panalibe ngakhale mmodzi amene anatha kumuyankha, ndipo kuchokera tsiku limenelo palibe amene analimbanso mtima kumufunsa mafunso.
-