Mateyu 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu! Chifukwa mukutseka Ufumu wakumwamba kuti anthu asalowemo. Popeza inuyo simukulowamo, mukuletsa amene akufuna kulowamo kuti asalowe.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2001, tsa. 213/15/1991, tsa. 510/1/1990, tsa. 23
13 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu! Chifukwa mukutseka Ufumu wakumwamba kuti anthu asalowemo. Popeza inuyo simukulowamo, mukuletsa amene akufuna kulowamo kuti asalowe.+