-
Mateyu 23:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Komanso mumati, ‘Ngati munthu watchula guwa lansembe polumbira, palibe kanthu, koma ngati munthu watchula mphatso imene ili paguwapo polumbira, asunge lumbiro lake.’
-