Mateyu 23:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu! Chifukwa muli ngati kapu ndi mbale zimene zatsukidwa kunja kokha+ koma mkati mwake muli mwakuda. Mkati mwa mitima yanu mwadzaza dyera*+ ndi kusadziletsa.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:25 Yesu—Ndi Njira, tsa. 254 Nsanja ya Olonda,9/15/2000, tsa. 19
25 Tsoka kwa inu alembi ndi Afarisi, anthu achinyengo inu! Chifukwa muli ngati kapu ndi mbale zimene zatsukidwa kunja kokha+ koma mkati mwake muli mwakuda. Mkati mwa mitima yanu mwadzaza dyera*+ ndi kusadziletsa.+