Mateyu 24:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano phunzirani zokhudza mtengo wa mkuyu kuchokera pa fanizo ili: Nthambi yake yanthete ikaphuka nʼkuchita masamba, mumadziwa kuti chilimwe chili pafupi.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:32 Yesu—Ndi Njira, tsa. 258 Nsanja ya Olonda,5/15/2003, tsa. 264/1/1990, tsa. 25
32 Tsopano phunzirani zokhudza mtengo wa mkuyu kuchokera pa fanizo ili: Nthambi yake yanthete ikaphuka nʼkuchita masamba, mumadziwa kuti chilimwe chili pafupi.+