Mateyu 24:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kumwamba ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mawu anga adzakhalapo mpaka kalekale.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:35 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, ptsa. 14-15, 20-21