Mateyu 24:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Koma dziwani izi: Ngati mwininyumba atadziwa nthawi imene wakuba angabwere,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti wakubayo athyole nʼkulowa mʼnyumba mwake.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:43 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, tsa. 14
43 Koma dziwani izi: Ngati mwininyumba atadziwa nthawi imene wakuba angabwere,+ angakhale maso ndipo sangalole kuti wakubayo athyole nʼkulowa mʼnyumba mwake.+