Mateyu 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho amene analandira matalente 5 uja anabwera ndi matalente ena owonjezera 5 nʼkunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente 5 koma onani, ndapindula matalente enanso 5.’+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:20 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 262-263 Nsanja ya Olonda,6/15/1995, tsa. 17
20 Choncho amene analandira matalente 5 uja anabwera ndi matalente ena owonjezera 5 nʼkunena kuti, ‘Ambuye, paja munandipatsa matalente 5 koma onani, ndapindula matalente enanso 5.’+