Mateyu 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+
29 Chifukwa aliyense amene ali nazo, adzapatsidwa zinanso zambiri ndipo adzakhala ndi zochuluka. Koma amene alibe adzalandidwa ngakhalenso zimene ali nazo.+