-
Mateyu 25:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Mitundu yonse ya anthu idzasonkhanitsidwa kwa iye ndipo adzalekanitsa anthu, mofanana ndi mmene mʼbusa amalekanitsira nkhosa ndi mbuzi.
-